Yeremiya 46:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anapunthwitsa ambiri, inde, anagwa wina pa mnzace, ndipo anati, Ukani, tinkenso kwa anthu athu, ku dziko la kubadwa kwathu, kucokera ku lupanga lobvutitsa.

Yeremiya 46

Yeremiya 46:6-19