Yeremiya 46:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Amitundu amva manyazi anu, dziko lapansi ladzala ndi kupfuula kwanu; pakuti amphamvu akhumudwitsana, agwa onse awiri pamodzi.

Yeremiya 46

Yeremiya 46:11-20