Yeremiya 45:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mau amene ananena Yeremiya mneneri kwa Baruki mwana wace wa Neriya, pamene analemba mau awa m'buku ponena Yeremiya, caka cacinai ca Yehoyakimu mwana wace wa Yosiya, mfumu ya Yuda, ndi kuti,

Yeremiya 45

Yeremiya 45:1-5