Yeremiya 44:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene tinafukizira mfumu yaikazi ya kumwamba, ndi kumthirira nsembe zothira, kodi tinamuumbira iye mikate yakumpembedzera, ndi kumthirira nsembe zothira, opanda amuna athu?

Yeremiya 44

Yeremiya 44:11-24