Yeremiya 44:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo amuna onse amene anadziwa kuti akazi ao anafukizira milungu yina, ndi akazi onse omwe anaimirirapo, msonkhano waukuru, anthu onse okhala m'dziko la Aigupto, m'Patirosi, anamyankha Yeremiya, kuti,

Yeremiya 44

Yeremiya 44:13-23