Yeremiya 44:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mau amene anadza kwa Yeremiya onena za Ayuda onse amene anakhala m'dziko la Aigupto, okhala pa Migidoli, ndi pa Tapanesi, ndi pa Nofi, ndi m'dziko la Patirosi, akuti,

Yeremiya 44

Yeremiya 44:1-2