Yeremiya 43:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye adzafika, nadzakantha dziko la Aigupto; nadzapereka kuimfa iwo a kuimfa, ndi kundende iwo a kundende, ndi kulupanga iwo a kulupanga.

Yeremiya 43

Yeremiya 43:8-13