Yeremiya 42:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cifukwa cace mumve mau a Yehova, Otsala inu a Yuda, atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli, Ngati mulozetsa nkhope zanu kuti mulowe m'Aigupto, kukakhala m'menemo;

Yeremiya 42

Yeremiya 42:8-20