Yeremiya 42:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akazembe onse a nkhondo, ndi Yohanani mwana wace wa Kareya, ndi Jezaniya mwana wace wa Hosiya, ndi anthu onse kuyambira wamng'ono, kufikira wamkuru, anayandikira,

Yeremiya 42

Yeremiya 42:1-5