Yeremiya 41:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu onse amene Ismayeli anatenga ndende kuwacotsa m'Mizipa anatembenuka nabwera, nanka kwa Yohanani mwana wace wa Kareya,

Yeremiya 41

Yeremiya 41:5-18