Yeremiya 40:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pamenepo Ayuda onse anabwerera kufumira ku malo onse kumene anawaingitsirako, nafika ku dziko la Yuda, kwa Gedaliya, ku Mizipa, nasonkhanitsa vinyo ndi zipatso zamalimwe zambiri.

Yeremiya 40

Yeremiya 40:11-16