Yeremiya 4:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mkango wakwera kuturuka m'nkhalango mwace, ndipo woononga amitundu ali panjira, waturuka m'mbuto mwace kuti acititse dziko lako bwinja, kuti midzi yako ipasuke mulibenso wokhalamo.

Yeremiya 4

Yeremiya 4:1-14