Yeremiya 4:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti anthu anga apusa, sandidziwa Ine; ali ana opulukira sazindikira; ali ocenjera kucita coipa koma kucita cabwino sakudziwa.

Yeremiya 4

Yeremiya 4:19-26