Yeremiya 39:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma aumphawi a anthu, amene analibe kanthu, Nebuzaradani kapitao wa alonda anawasiya m'dziko la Yuda, nawapatsa mipesa ndi minda nthawi yomweyo.

Yeremiya 39

Yeremiya 39:3-18