Yeremiya 38:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu Zedekiya anati kwa Yeremiya, Ine ndiopa Ayuda amene anandipandukira ine kunka kwa Akasidi, angandipereke ine m'manja mwao, angandiseke.

Yeremiya 38

Yeremiya 38:18-27