Yeremiya 37:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Zedekiya mfumu anatuma Yehukali mwana wa Selemiya, ndi Zefaniya mwana wa Maseya wansembe, kwa Yeremiya mneneri, kukanena, Mutipemphereretu kwa Yehova Mulungu wathu.

Yeremiya 37

Yeremiya 37:1-11