Yeremiya 37:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pokhala iye m'cipinda ca Benjamini, kapitao wa alonda anali kumeneko, dzina lace Iriya, mwana wa Selemiya, mwana wa Hananiya; ndipo iye anamgwira Yeremiya mneneri, nati, Ulinkupandukira kwa Akasidi.

Yeremiya 37

Yeremiya 37:6-14