Yeremiya 36:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Baruki mwana wa Neriya anacita monga mwa zonse anamuuza iye Yeremiya mneneri, nawerenga m'buku mau a Yehova m'nyumba ya Yehova.

Yeremiya 36

Yeremiya 36:1-13