Yeremiya 36:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo za Yehoyakimu mfumu ya Yuda uziti, Yehova atero: Iwe watentha mpukutu uwu, ndi kuti, Bwanji walemba m'menemo, kuti, Mfumu ya ku Babulo idzadzadi nidzaononga dziko ili, nidzatha m'menemo anthu ndi nvama?

Yeremiya 36

Yeremiya 36:22-30