Yeremiya 36:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu inauza Yeremeeli mwana wace wa mfumu, ndi Seraya mwana wa Azirieli, ndi Selemiya mwana wa Abidieli, kuti awagwire Baruki mlembi ndi Yeremiya mneneri; koma Yehova anawabisa.

Yeremiya 36

Yeremiya 36:23-29