Yeremiya 36:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tenga buku lampukutu, nulembe m'menemo mau onse ndanena kwa iwe akunenera Israyeli, ndi akunenera Yuda, ndi akunenera amitundu onse, kuyambira tsiku ndinanena kwa iwe, kuyambira masiku a Yosiya, mpaka lero.

Yeremiya 36

Yeremiya 36:1-10