Yeremiya 34:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mau amene anadza kwa Yeremiya kucokera kwa Yehova, atapangana Zedekiya pangano ndi anthu onse amene anali pa Yerusalemu, kuti awalalikire iwo ufulu;

Yeremiya 34

Yeremiya 34:7-17