Yeremiya 34:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma mwabwerera ndi kuipitsa dzina langa, ndi kubwezera m'ukapolo yense kapolo wace wamwamuna, ndi wamkazi, amene munammasula akacite zao, ndipo munawagonjetsa, akhale akapolo anu amuna ndi akazi.

Yeremiya 34

Yeremiya 34:10-22