Yeremiya 34:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo akuru onse ndi anthu onse anamvera, amene anapangana mapangano, akuti yense ammasule kapolo wace wamwamuna, kapena wamkazi osawayesanso akapolo; iwo anamvera nawamasula;

Yeremiya 34

Yeremiya 34:1-16