Yeremiya 33:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kodi sulingalira comwe anena anthu awa, kuti, Mabanja awiri amene Yehova anawasankha, wataya iwo? comweco anyoza anthu anga, kuti asakhalenso mtundu pamaso pao.

Yeremiya 33

Yeremiya 33:17-26