Yeremiya 32:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anandipatsa Ine mbuyo, si nkhope, ngakhale ndinawaphunzitsa, kuuka m'mamawa ndi kuwaphunzitsa, koma sanamvera kulangizidwa.

Yeremiya 32

Yeremiya 32:29-38