Yeremiya 32:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ana a Israyeli ndi ana a Yuda anacita zoipa zokha zokha pamaso panga ciyambire ubwana wao, pakuti ana a Israyeli anandiputa Ine kokha kokha ndi nchito ya manja ao, ati Yehova.

Yeremiya 32

Yeremiya 32:29-32