Yeremiya 32:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo analowa, nakhalamo; koma sa namvera mau anu, sanayenda m'cilamulo canu; sanacita kanthu ka zonse zimene munawauza acite; cifukwa cace mwafikitsa pa iwo coipa conseci;

Yeremiya 32

Yeremiya 32:20-31