Yeremiya 32:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo munaturutsa anthu anu Israyeli m'dziko la Aigupto ndi zizindikiro, ndi zodabwitsa, ndi dzanja lamphamvu, ndi mkono wotambasuka, ndi mantha ambiri;

Yeremiya 32

Yeremiya 32:14-26