Yeremiya 32:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ha! Yehova Mulungu, taonani, Inu munalenga kumwamba ndi dziko lapansi ndi mphamvu yanu yaikuru ndi mkono wanu wotambasuka; palibe cokulakani Inu;

Yeremiya 32

Yeremiya 32:13-19