Yeremiya 32:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mau amene anadza kwa Yeremiya kucokera kwa Yehova caka cakhumi ca Zedekiya mfumu ya Yuda, cimene cinali caka cakhumi ndi cisanu ndi citatu ca Nebukadirezara.

Yeremiya 32

Yeremiya 32:1-9