Yeremiya 31:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndidzamangitsanso mudzi wako, ndipo udzamangidwa, iwe namwali wa Israyeli; udzakometsedwanso ndi mangaka, ndipo udzaturukira masewero a iwo akukondwerera.

Yeremiya 31

Yeremiya 31:1-6