Yeremiya 31:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

si monga pangano limene ndinapangana ndi makolo ao tsiku lija ndinawagwira manja kuwaturutsa m'dziko la Aigupto; pangano langa limenelo analiswa, ngakhale ndinali mbuyao, ati Yehova.

Yeremiya 31

Yeremiya 31:25-40