Yeremiya 31:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma yense adzafa cifukwa ca mphulupulu yace; yense amene adya mphesa zowawa, mano ace adzayayamira.

Yeremiya 31

Yeremiya 31:20-36