Yeremiya 31:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli, Kawirinso adzanena mau awa m'dziko la Yuda ndi m'midzi yace, pamene ndibwezanso undende wao; Yehova akudalitse iwe, wokhalamo cilungamo, iwe phiri lopatulika.

Yeremiya 31

Yeremiya 31:21-25