Yeremiya 30:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Funsani tsopano, ndi kuona ngati mwamuna aona mwana; cifukwa canji ndiona mwamuna ndi manja ace pa cuuno cace, monga mkazi alinkubala, ndi nkhope zao zotumbuluka?

Yeremiya 30

Yeremiya 30:1-14