Yeremiya 3:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mau amveka pa mapiri oti se, kulira ndi kupempha kwa ana a Israyeli; pakuti anaipitsa njira yao, naiwala Yehova Mulungu wao.

Yeremiya 3

Yeremiya 3:18-23