Yeremiya 3:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo padzaoneka, pamene mudzakhala ambiri ndi kucuruka m'dzikomo masiku awo, ati Yehova, sadzatinso konse, Likasa la cipangano ca Yehova; silidzalowa m'mtima; sadzalikumbukira; sadzanka kukaliona, sadzacitanso konse.

Yeremiya 3

Yeremiya 3:14-23