Yeremiya 3:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma bvomereza zoipa zako, kuti walakwira Yehova Mulungu wako, ndi kupatukira mwa alendo patsinde pa mitengo yaiwisi yonse, ndipo sunamvera mau anga, ati Yehova.

Yeremiya 3

Yeremiya 3:6-16