Yeremiya 29:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

popeza watitumizira mau ku Babulo, akuti, Undende udzakhalitsa; mangani nyumba, khalani m'menemo; limani minda, idyani zipatso zao?

Yeremiya 29

Yeremiya 29:27-32