Yeremiya 29:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cifukwa anacita zopusa m'Israyeli, nacita cigololo ndi akazi a anansi ao, nanena mau onama m'dzina langa, amene ndinawauza kuti asanene; Ine ndine wodziwa, ndi mboni, ati Yehova.

Yeremiya 29

Yeremiya 29:15-31