Yeremiya 27:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

zimene sanazitenga Nebukadinezara mfumu ya ku Babulo, pamene anamtenga ndende Yekoniya mwana wace wa Yehoyakimu, mfumu ya Yuda, kucokera ku Yerusalemu kunka ku Babulo; ndi akuru onse a Yuda ndi Yerusalemu;

Yeremiya 27

Yeremiya 27:11-22