Yeremiya 27:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Musamvere mau a aneneri amene anena ndi inu, kuti, simudzamtumikira mfumu ya ku Babulo; pakuti akunenerani zonama.

Yeremiya 27

Yeremiya 27:12-17