Yeremiya 27:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinanena kwa Zedekiya mfumu ya Yuda monga mau onse amenewa, kuti, Longani makosi anu m'gori la mfumu ya ku Babulo, ndi kumtumikira iye ndi anthu ace, ndipo mudzakhala ndi moyo.

Yeremiya 27

Yeremiya 27:10-20