Yeremiya 27:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Poyamba kukhala mfumu Yehoyakimu mwana wace wa Yosiya, mfumu ya Yuda, mau awa anadza kwa Yeremiya kucokera kwa Yehova, kuti,

Yeremiya 27

Yeremiya 27:1-8