Yeremiya 26:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Yeremiya ananena kwa akuru onse ndi kwa anthu onse, kuti, Yehova anandituma ine ndinenere nyumba iyi ndi mudzi uwu mau onse amene mwamva.

Yeremiya 26

Yeremiya 26:9-21