Yeremiya 25:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Phokoso lidzadza ku malekezero a dziko lapansi; pakuti Yehova ali ndi mlandu ndi mitundu ya anthu, adzatsutsana ndi anthu onse; koma oipa, adzawapereka kulupanga, ati Yehova.

Yeremiya 25

Yeremiya 25:24-34