Yeremiya 25:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi mafumu onse a kumpoto, a kutari ndi a kufupi, wina ndi mnzace; ndi maufumu onse a dziko lapansi, okhala pansi pano; ndi mfumu ya Sesaki adzamwa pambuyo pao.

Yeremiya 25

Yeremiya 25:25-28