Yeremiya 25:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndiponso ndidzawacotsera mau akusekera ndi mau akukondwera, ndi mau a mkwati, ndi mau a mkwatibwi, mau a mphero, ndi kuwala kwa nyali.

Yeremiya 25

Yeremiya 25:8-20