Yeremiya 25:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mau amene anadza kwa Yeremiya za anthu onse a Yuda caka cacinai ca Yehoyakimu mwana wace wa Yosiya, mfumu ya Yuda; ndico caka coyamba ca Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo;

Yeremiya 25

Yeremiya 25:1-11